Home » National » ANTHU AKWA CHIMWALA AKANA KULANDIRA NDALAMA ZA MTUKULA PAKHOMO
ANTHU AKWA CHIMWALA AKANA KULANDIRA NDALAMA ZA MTUKULA PAKHOMO

ANTHU AKWA CHIMWALA AKANA KULANDIRA NDALAMA ZA MTUKULA PAKHOMO

By Cul Prince

ANTHU AKWA CHIMWALA AKANA KULANDIRA NDALAMA ZA MTUKULA PAKHOMO

Panali kusamvana pakati pa anthu olandira ndalama za mtukula pakhomo ndi akuluakulu olandiritsa ndalama ochokera kuboma.

Nkhani yonse inayambira pomwe m’modzi mwa akuluakulu ochokera kubomawa anauza anthu odzalandira ndalamawa kuti ndalama zomwe angalandire patsikulo ndi zomwe akhala akulandira m’mbuyomo.

Izi sizinasangalatse anthuwa, atafunsa chifukwa chomwe chinapangitsa zonsezo, iwo ananena kuti kwinako anawaonjezera (anaonjezeredwa 50,000 aliyense) pama centre ena omwe ali mderali (Kasolo ndi Changamire). Kusamvana kunabuka pakati pa maguluwa (olandiritsa ndi olandira ndalama). Kenaka anthu olandira ndalama aja anayamba kuimba nyimbo amvekere “sitilora sitilora” ndipo olandiritsa ndalama ananyamuka pamalopo. Anthuwa akonza mkumano ofuna kukumana ndi Bwana Mkubwa wabomali M’busa Moses Owen Chimphepo kuti akambirane za nkhaniyi,

Madera ambiri analandira ndalama zokwelerapo (K50,000 aliyense) pamwamba pa ndalama zomwe akhala akulandira.

Malawi Freedom Network
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  
 •  

About malawi

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

*

x

Check Also

Child Rights Organization Appeal for Support

Child Rights Organization Appeal for Support

Dowa Lodge To Have Water Tank Fence

DOWA LODGE TO HAVE WATER TANK, FENCE

Machinga Concerned Residents Wants DC Out

MACHINGA CONCERNED RESIDENTS WANTS DC OUT

error

Share Breaking News