Thursday, March 28
Shadow

Tag: Democratic Progressive Party

Chipani Cha DPP Chati Chodabwa Kuti Police Sinamange Wina Aliyense Pa Zipolowe Za Ku Lilongwe

Chipani Cha DPP Chati Chodabwa Kuti Police Sinamange Wina Aliyense Pa Zipolowe Za Ku Lilongwe

News, Politics
Chipani cha Democratic Progressive Party _ DPP chati chikudabwa kuti mpaka pano a polisi sanamangepo munthu wina aliyese yemwe akukhudzidwa ndi zachipongwe zomwe otsatila chipani cha MCP anapangira otsatila Chipani cha DPP ku Lilongwe pa mbowe filling station. Nkulu osutsa boma kunyumba ya Malamulo a Mary Navicha, ati akudabwa nazo kuti apolisi akugwiritsidwa ntchito ngati achipani m'malo mogwira ntchito yawo yopeleka chitetezo. Chipongwe Chochitika Lachisanu koma mpaka pano palibe yemwe wanjatidwa. " Ngati a Chakwera akuzitengela Masewera izi zitha kuzayambitsa Nkhondo m'dziko muno" Anatero a Navicha. A Navicha anapitilira kunena kuti " Ngati chipani cha DPP tiliso ndi kuthekera koti tikhoza kukwanitsa zomwe akupanga a MCP ku m'chigawo chapakati chawo chomwe koma ife timakonda Mten...
President Lazarus Chakwera has officially opened the Blantyre International Cancer Centre, The private health facility, has been constructed by the Thomson and Barbara Mpinganjira Foundation