Malawi Freedom Network
Giving you daily news that rock the world
FeaturedSports

titha Kutembenuza Tebulo

Timu ya Civo United yati ili ndi kuthekera kodzidzimutsa timu ya FCB Nyasa Big Bullets nkuitulutsa mu mpikisano wa Airtel Top 8 pa masewero omwe alipo masanawa pa bwalo la Civo.

Mphunzitsi wa timuyi Abas Makawa wati anyamata ake akonzeka ndipo otsatira timuyi abwere adzaone chipambana chawo.

Koma ku mbali ya timu ya FCB Nyasa Big Bullets, Callisto Pasuwa wati akudziwa bwino lomwe mphamvu ya timu ya Civo ndipo akudziwa bwino mothanirana nayo.

Awa ndi masewero achibwereza ndipo matimu awiriwa atakumana koyamba pa bwalo la Kamuzu, Bullets idapambana 2-0.

Wopambana masewerowa akuyembekezeka kukumana ndi wopambana pakati pa Kamuzu Barracks ndi Chitipa United omwe akumane mawa, masewero womwe Chitipa United ikutsogola 2-0 kuchokera m’masewero woyamba.

Related posts

A Chakwera Adzudzula Ogwiritsa ntchito imfa ya Chilima pa ndale

Malawi Freedom Network

Analysis: Joyce Banda’s Political Strategy and New Partnerships Ahead of 2025 Elections

By Burnett Munthali

Barcelona sweating on Dani Olmo’s fitness after Spain coach confirms ‘bad knock’

Malawi Freedom Network

Barcelona consider offering an extension to 22-year-old starlet after debut vs Valencia

Malawi Freedom Network

APM Announces DPP’s Alliance with AFORD, UTM, and UDF for 2025 Election

By Burnett Munthali

UTM Convention Slated November 7

Malawi Freedom Network

Leave a Comment

* By using this form you agree with the storage and handling of your data by this website.

Leave a review

This website uses cookies to improve your experience. We'll assume you're ok with this, but you can opt-out if you wish. Accept Read More