EURO Semi-Final Results:

Timu ya Spain yafika ndime yomaliza ya mpikisano wa Euro wa chaka chino itagonjetsa timu ya France ndi zigoli ziwiri kwa chimodzi.

Zateremu ndekuti Spain ikuyembekezeka kusewera ndi opambana pa masewero apakati pa England ndi Netherlands omwe akhale akuseweredwa lachitatu.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *