Malamulo akumulola Chilima -UTM

Chipani cha UTM chatsutsa malipoti akuti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino yemweso ndi mtsogoleri wa chipanichi,Saulos Chilima sali woyenera kudzapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri wa dziko pa chisankho cha chaka cha m’mawa.

Izi zikudza pomwe anthu ambiri pa masamba a m’chezo akhala akuyankhula kuti Chilima sali woyenera kudzaimira nawo pa mpando wa utsogoleri wa dziko lino malingana ndi malamulo.

Koma m’neneri wa chipanichi, Felix Njawala wawuza Timveni Online kuti malamulo akumulola Chilima ngakhale wakhala wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino kwa materemu awiri.

Njawala wati pali anthu ena omwe akufalitsa nkhanizi mwadala ndi cholinga chongofuna kusokoneza komanso kuchotsa chidwi cha a Malawi pa a Chilima.

Related Posts

DPP Blues Rebels Brings Division In

The way Charles Mchacha is castigating the Leader of Opposition in Parliament, Hon Kondwani Nankhumwa, is just testimony enough that Read more

Malawi Freedom Network advice President Banda to fight corruption

If you thought Malawians are lazy people, I bet you a Dinosaur, think twice and you will know, check in Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

David Bisnowaty former Member Of Parliament for Lilongwe City Centre break silence on political situation in the country

Political cum and former Member Of Parliament for Lilongwe City Centre break silence on political situation in the country https://youtu.be/S20UYlVcHs8

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window