---
title: "NDIKUFUNA NANKHUMWA AZIMUGWADIRA MUTHARIKA-Namalomba"
url: "https://malawifreedomnetwork.com/plans-to-ride-out-hurricane-the-florence-on-a-boat/"
description: "ShareMneneri wa Chipani cha DPP a Shadreck Namalomba,awunza Kondwani Nankhumwa kuti asamapange ziganizo payekha akafuna kuchita zinthu. A Namalomba ati,Nankhumwa akamafuna kuchita chinthu chokhuzana ndi mu chipani cha DPP, aziyamba amufusa kale mtsogoleri wa Chipanichi a Mutharika kamba koti iye ndi wamkulu. Namalomba amalankhula izi ku mkumano womwe udaliko dzulo ku Mangochi. A Namalomba ,awunza…"
author: "Malawi Freedom Network"
published: "2026-07-24T16:17:41+00:00"
modified: "2026-07-24T19:21:30+00:00"
language: "en-US"
type: "post"
site: "Malawi Freedom Network"
word_count: 74
---

# NDIKUFUNA NANKHUMWA AZIMUGWADIRA MUTHARIKA-Namalomba

Mneneri wa Chipani cha DPP a Shadreck Namalomba,awunza Kondwani Nankhumwa kuti asamapange ziganizo payekha akafuna kuchita zinthu.

A Namalomba ati,Nankhumwa akamafuna kuchita chinthu chokhuzana ndi mu chipani cha DPP, aziyamba amufusa kale mtsogoleri wa Chipanichi a Mutharika kamba koti iye ndi wamkulu.

Namalomba amalankhula izi ku mkumano womwe udaliko dzulo ku Mangochi.

A Namalomba ,awunza anthu kuti a Nankhumwa ndi munthu wotsokoneza mu chipani ndipo Peter Mutharika,ndiwokhumudwa ndi zomwe Nankhumwa akuchita.“\`

---

Source: Malawi Freedom Network — https://malawifreedomnetwork.com/plans-to-ride-out-hurricane-the-florence-on-a-boat/
