UTM ikhala ndi msonkhano wosankha adindo pa 17 Nov
Chipani cha United Transformation Movement-UTM chatsimikiza kuti chichititsa msonkhano wake waukulu wosankha adindo achipanichi (Convention) pa 17 November chaka chino. Mneneri wa chipanichi Felix Njawala ndiye wanena izi pa mkumano…









