---
title: "PP yayaka moto kuti buu"
url: "https://malawifreedomnetwork.com/pp-yayaka-moto-kuti-buu/"
description: "Share President wa chipani cha Peoples Party yemweso ndi m’tsogoleri wopuma wa dziko lino, Mayi Joyce Banda wati mu nthawi ya ulamuliro wawo zinthu m’dziko muno zinkayenda bwino, palibe ankavutika ndi njala komanso anthu sankagona pa filling station. A Banda ati ndi chipani chawo chokha chomwe chinabweletsa magetsi osazima mu mdziko muno. Share"
author: "Suleman Chitera"
published: "2026-07-24T16:17:50+00:00"
modified: "2026-07-24T19:21:22+00:00"
language: "en-US"
type: "post"
site: "Malawi Freedom Network"
word_count: 51
image: "https://malawifreedomnetwork.com/wp-content/uploads/2024/09/FB_IMG_1725675634499.jpg"
categories:
  - "Breaking News"
---

# PP yayaka moto kuti buu

President wa chipani cha Peoples Party yemweso ndi m’tsogoleri wopuma wa dziko lino, Mayi Joyce Banda wati mu nthawi ya ulamuliro wawo zinthu m’dziko muno zinkayenda bwino, palibe ankavutika ndi njala komanso anthu sankagona pa filling station.

A Banda ati ndi chipani chawo chokha chomwe chinabweletsa magetsi osazima mu mdziko muno.

---

Source: Malawi Freedom Network — https://malawifreedomnetwork.com/pp-yayaka-moto-kuti-buu/
