Sunday, October 1Malawi's top news source
Shadow

Tag: Sugar

M’tengo wa pakete imodzi ya shuga, tsopano ukumafanana ndi wa bread m’modzi

M’tengo wa pakete imodzi ya shuga, tsopano ukumafanana ndi wa bread m’modzi

Local
Izi zadza chifukwa bread wakwela mtengo kufika pa 1 000 Kwacha m'modzi , m'magolosale ena. Akuluakulu ena omwe ali ndi ma bakery, akuti mtengo wa tiligu, wakwela padziko lonse, zomwe zachititsanso kukwela kwa mtengo wa ufa opangila bread. "Chomcho , ufa wopangila bread wachoka pa 36, 000 Kwacha kufika pa 48, 000 Kwacha , thumba limodzi la 50 kilograms," watelo m'modzi mwa iwo. Ndipo m'kulu wa bungwe la ogula malonda la Consumers Association of Malawi - CAMA, a John Kapito, wati boma lichitepo kanthu pa nkhani ya mitengoyi, chifukwa anthu m'dziko lino, avutika. ```