---
title: "Zomwera Tea? Zilipo Zonse Kuno – Makonda Makonda!"
url: "https://malawifreedomnetwork.com/zomwera-tea-zilipo-zonse-kuno-makonda-makonda/"
description: "Share Inu mmakonda chani Akasi? Zonse zilipo ndipo zili bwino kwambiri! Kaya mukufuna baked treats kapena natural farm-fresh snacks, Ekhaya Farms Foods yakonzeratu zonse zomwe mungafune! Timanyadira kukupatsani zakudya zomwe zimakwatiro bwino ndi tiyi nthawi iliyonse – kaya nkumawa, masana kapena madzulo. Baked Treats? Tili nazo! Zopangidwa ndi chikondi Zofewa komanso zokoma Zosiyanasiyana kuti musankhe…"
author: "Suleman Chitera"
published: "2026-07-24T16:17:59+00:00"
modified: "2026-07-24T19:21:10+00:00"
language: "en-US"
type: "post"
site: "Malawi Freedom Network"
word_count: 77
image: "https://malawifreedomnetwork.com/wp-content/uploads/2025/05/IMG-20250509-WA0772.jpg"
categories:
  - "Breaking News"
  - "Business"
---

# Zomwera Tea? Zilipo Zonse Kuno – Makonda Makonda!

Inu mmakonda chani Akasi? Zonse zilipo ndipo zili bwino kwambiri! Kaya mukufuna baked treats kapena natural farm-fresh snacks, Ekhaya Farms Foods yakonzeratu zonse zomwe mungafune!

Timanyadira kukupatsani zakudya zomwe zimakwatiro bwino ndi tiyi nthawi iliyonse – kaya nkumawa, masana kapena madzulo.

Baked Treats? Tili nazo!

Zopangidwa ndi chikondi

Zofewa komanso zokoma

Zosiyanasiyana kuti musankhe zomwe mumakonda

Ekhaya Farms Foods – Zakudya Zachilengedwe. Zakudya Zanu.

Pitani lero! Mukachite enjoy Tea time ndi Zomwera za makonda!

# ZomweraTea

# MakondaMakonda

# BakedTreats

# EkhayaFarmsFoods

# SnackTimeZokoma

---

Source: Malawi Freedom Network — https://malawifreedomnetwork.com/zomwera-tea-zilipo-zonse-kuno-makonda-makonda/
