Boma Ndi lomweli–Kabwila

FB IMG 1730941673502

Chipani cha Malawi Congress (MCP) chati zipani zotsutsa boma m’dziko muno zisatengeke ndi zomwe zachitika ku America komwe chipani cholamula cha Democratic chagonja pa chisankho, poganiza kuti izi zichitikanso kuno ku mudzi pa chisankho cha chaka cha mawa.

Mneneri wa MCP, Jessie Kabwila wati zina mwa zomwe zagwetsa Democratic Party zomwe ndi kuphatikizapo mavuto a za chuma, zikukonzedwa kale ndi boma la Chipani chawo, zomwe aMalawi ndi mboni.

Apa, iye watsindika kuti MCP sikutuluka m’boma chaka cha mawa chifukwa ulamuliro wake ukukondedwa ndi anthu kaamba koyika chidwi cha miyoyo yawo patsogolo.

0 0 votes
Article Rating
Subscribe
Notify of
guest
0 Comments
Oldest
Newest Most Voted
Inline Feedbacks
View all comments
//otieu.com/4/9370459
0
Would love your thoughts, please comment.x
()
x