Tuesday, March 19
Shadow

Exclusive

Zikhale Extensively Consult On CDF-Education Funding

Zikhale Extensively Consult On CDF-Education Funding

Education, Exclusive, Featured
Homeland Security Minister, Ken Zikhale Ng'oma who is also member of parliament for Nkhata-Bay South constituency has challenged Head-teachers, and Primary Education Advisors (PEA) drawn from all the three zones of his constituency to continue working hard in order to sustain quality education. The Saturday meeting centred on key issues affecting quality service delivery in the education sector in Nkhata-Bay South constituency such as a huge need for more teachers houses, schools blocks, and other pertinent teaching and learning materials. In an interview with the Malawi Daily Telegraph, the Homeland Security Minister emphasized on the need to involve key stakeholders in decision-making on how best to use the Constituency Development Fund (CDF). It is against this background that...

Tidkira Tsiku Lomwe Ayambe Kupanga Zipatso Zoyendera-CDEDI

Exclusive, Local
Bungwe la Centre for Democracy and Economic Development initiatives-CDEDI lati lidikirabe tsiku lomwe nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka iyambe ntchito yake yopanga ziphaso(Passport). Komabe mkulu wa bungweli,Sylvester Namiwa wati wokondwera ndi ganizo la nthambi yoona zolowa ndi kutuluka potsitsa mtengo wa e-passport. Namiwa wati ngakhale ali wokondwa ndi kutsika mtengo wa chiphaso , iye wati ganizo lotsitsa mtengo wa chiphasochi limayenera kuchitika pa nthawi yomwe boma linathetsa mgwirizano wake ndi kampani ya Techno Brain. Nthambi yoona zolowa ndi kutuluka yalengeza kuti ntchito yopanga ziphaso iyambiraso sabata ino.
Ndondomeko Za Chuma Sizikuyendabwino–Mwanamveka

Ndondomeko Za Chuma Sizikuyendabwino–Mwanamveka

Exclusive, Local
Chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) ndi chomwe chayamba kuyankhulapo pa ndondomeko ya za chuma ya mchaka cha 2024 mpaka 2025 yomwe inapelekedwa ku nyumba ya malamulo pa 23 February 2024. Phungu wa dera la ku m'mwera kwa boma la Chiradzulu, yemwenso wasankhidwa ngati m'neneri wa Chipani cha DPP pa nkhani za chuma, Joseph Mwanavemkha wati boma lalephera kufotokoza bwino komwe lipeze ndalama zomwe liyendetsere ndondomeko ya za chumayi. Malingana ndi Mwanavemkha, bungwe lotolela misonkho mdziko muno likuvutika ndi kale kutolela misonkho kamba kakuti chuma sichikuyenda bwino. Mwanavemkha wati ndondomekoyi ipangitsa kuti ma business ambiri atsekedwe chifukwa cha ku chuluka kwa misonkho. Iye wachenjezaso kuti dziko lino liyembekezere kuti chuma cha dziko lino chipitilira k...
Teachers urged to get professional license

Teachers urged to get professional license

Education, Exclusive, Featured
Ministry of Education has reminded all teachers in the country to get registered with Teachers Council of Malawi (TCM) and get a license if they are to remain in the profession. Speaking in an interview on Friday, Spokesperson in the Ministry, Mphatso Nkuonera said registration for licensing is currently underway and come July 1, 2024 all unlicensed teachers will be barred from practicing in accordance with Education Act of 2013. In its second board meeting held on 21st December, 2023, the Teachers Council approved guidelines of teacher indexing, registration, and licensing. The guidelines mandate all student and serving teachers to be registered with the council for them to practice. “All institutions are therefore requested to inform all serving primary school teachers, seconda...
Chakwera Aonetse Kuti Siwolephera Kutumikira A Malawi

Chakwera Aonetse Kuti Siwolephera Kutumikira A Malawi

Exclusive, Featured
Mabungwe omwe si aboma ku Kasungu ati nthawi yakwana tsopano kuti mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera aonetse kuti siwolephera kutumikira a Malawi. Wapampando wa mabungwewa a Braxton Banda wati a Chakwera akuyenera kuchotsa ntchito mkulu wa nthambi ya immigration a Charles Kalumbo pa chimpwirikiti chokhudza ma passport. A Banda akukhulupilira kuti izi zithandizira kuti anthu asataye chikhulupiliro mwa utsogoleri wa a Chakwera maka pomwe chisankho cha chaka cha mawa chayamba kale kununkhira. "Kulephera kulondoloza ndikupezanso mayankho a vuto lomwe lili ku nthambi ya immigration, anthu ena akuloza chala mtsogoleri wa dziko linoyu. "Ichi ndi chifukwa chake ife a mabungwe tikuwapempha komanso kuwatsina khutu a pulezidenti kuti achotse ntchito mkuluyu, pofuna kuteteza mbir...
Misinformation Bites Chakwera, Opens IBCC

Misinformation Bites Chakwera, Opens IBCC

Exclusive, Featured, News
BY: DRAXON MALOYA President Lazarus Chakwera stood and resolute as he addressed the crowd with a solemn expression on his face denouncing the malicious propaganda spreading like wildfire throughout the country that he is the cause of hunger and economic challenges affecting Malawians. The solemn expression comes against the background of some opposition political leaders conducting motor parades condemning him and the Tonse Alliance government for the hunger and economic instability affecting people’s livelihoods. Speaking on Tuesday when presiding over the opening of the multi-billion Kwacha state-of-the-art International Blantyre Cancer Centre (IBCC) constructed by the Thomson and Barbra Mpinganjira Foundation, Chakwera said it is sad that that he is being insulted for even the...
Chakwera Inaugurates International Cancer Centre in Blantyre

Chakwera Inaugurates International Cancer Centre in Blantyre

Exclusive, Featured, Health
Cancer patients in the country can now breath a sign following the inauguration of mult billion kwacha cancer centre, the international Blantyre cancer Centre-IBCC which will now give access to advanced treatment. Speaking during the official launch in Nyambadwe, Blantyre, President Lazarus Chakwera has underscored the magnificent role that the cancer centre will play in the country to make cancer treatment accessible to Malawians. Chakwera said the battle to defeat cancer requires a concerted effort, as the disease does not segregate anyone; hence, the facility is very important. He also applauded the Thomson and Barbara Mpinganjira Foundation for the construction of the Cancer Center, which he said will ease the burden of the disease on Malawians. He therefore urged the Min...
Chipani chatsopano Cha N D P Achikhazikitsa Mdzikolino

Chipani chatsopano Cha N D P Achikhazikitsa Mdzikolino

Exclusive, Featured, Politics
Chipani chatsopano chomwe akuchitcha National Development Party (NDP) ndipo mtsogoleri wake ndia Frank Mwenefumbo achikhazikitsa mdzikolino. Ofesi ya mkulu oona zakalembera wa zipani zandale yapeleka kale chilolezo ku chipanichi kuti chitha kuyamba kugwira ntchito zake mdzikolino kuyambira pa 1 March, 2024. Mlembi wamkulu wachipanichi a Gerald Chilongo watsimikiza lero kuti chipanichi achikhazikitsa mwazina pofuna kugwira ntchito ndi a Malawi polimbana ndimavuto monga a zachuma komanso kusakazika kwa zachilengedwe. Komabe a Chilongo ati pakadalipano chipanichi chaika chidwi polimbikitsa nthambi zake ndipo pakadalipano sichidapange chiganizo ngati chizapange mgwilizano ndi zipani zina kapena ayi. Mtsogoleri wachipanichi a Mwenefumbo, anakhalapo mneneri wachipani cha UTM.
President Lazarus Chakwera has officially opened the Blantyre International Cancer Centre, The private health facility, has been constructed by the Thomson and Barbara Mpinganjira Foundation