Wothandizira Episikopi Wa Lilongwe Apempha Akhristu A Mipingo Ya Katolika Kuti Azipembedza Ukaristia
Wolemba: Mabvuto Kalawa, Malawi Freedom Network Wothandizira Episkopi wa Mpingo wa Katolika mu Lilongwe, Bishop Vincent Mwakhwawa, wapempha Akhristu a ku Nathenje Parish kuti azikumbukira kupembedza Ukaristia nthawi zonse. Bishop…









