Dalitso Kabambe ndi Yankho Lathu la 2030: “Sitifunanso Kulakwisanso,” Atero Amalawi
Olemba Mtolankhani Wathu Amalawi ambiri akuyamba kulankhula momveka bwino za tsogolo la dziko lawo pamene chisankho cha 2030. M’mawu omwe akufalikira m’misonkhano, m’mabwalo a pa intaneti komanso m’macheza a tsiku…








