STATE HOUSE ILENGEZA IMFA YA MIRIAM CHAKWERA

“`President Lazarus Chakwera wataya mlongo wawo Mirriam Chakwera yemwe wamwalira lero.

Mlembi wa atolankhani a President Anthony Kasunda walengeza za imfa ya mlongo wake wa Chakwera mwachidule.

A Kasunda adaonjeza kuti Chakwera wathetsa nthawi yomweyo zokambirana zake ndi anthu.
ā€œMtsogoleri wa dziko lino ayambiranso zokambirana zake ndi anthu akayika maliro a mlongo wawo, zomwe zikuyenera kuchitika pa Epulo 20 mā€™mudzi mwa Manase ku Mdika mā€™boma la Dowa,ā€ adatero Kasunda.“`

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Please disable your adblocker or whitelist this site!