Mabedi Wapempha Kugwirana Manja
Mphunzitsi wa timu ya mpira wamiyendo ya dziko lino, Patrick Mabedi, wapempha boma komanso makampani omwe siaboma kuti agwirane manja…
News from Malawi you can trust
Mphunzitsi wa timu ya mpira wamiyendo ya dziko lino, Patrick Mabedi, wapempha boma komanso makampani omwe siaboma kuti agwirane manja…
Beach Soccer Association (BSA) yati chipambano chimene angachipeze pa mawa, loweruka, pamene akukumana ndi timu ya Burundi mu masewero odzigulira…
Masewero onse atatu omwe analipo lero, lachitatu mu ligi ya TNM athera kufanana mphamvu. Civo United yafananitsa mphamvu ndi Mighty…
Timu ya Baka City yalandira mtibu wa zigoli zokwana zinayi kwa duu pamasewero omwe amasewera ndi Premier Bet Dedza Dynamos.…
A match between Moyale Barracks and Bangwe All Stars in TNM Super League ended in controversy after the hosts, the…
BY DRAXON MALOYA Mzuzu, Malawi – The TNM Super League match between Moyale Barracks FC and Bangwe All-Stars at Mzuzu…
Super League of Malawi (Sulom) yati pakuyenera kuikidwa ndondomeko yapadera ndi cholinga choti matimu komanso bungweli adzipindula pa phindu lomwe…
Timu ya mpira wa pagombe ya dziko lino ya Beach Soccer muchingerezi yagonjetsa timu ya Burundi 7-6 mu nzinda wa…
Fading TNM Defending Champions, FCB Nyasa Big Bullets continue their poor form when they were beaten by Karonga United 2-1…
Timu ya mpira wa pagombe ya dziko lino, Beach Soccer mu chingelezi, yanyamuka m’dziko muno ulendo wa ku Bujumbura m’dziko…