Tithamangire kwa Mulungu osati kunyanyala- Mpima.
Bungwe la Coaches Association of Malawi yalangiza mamembala ake kuti adzikhala oleza mtima pomwe akugwira ntchito yawo kupewa kupanga ziganizo zolakwika. Bungweli layankhula kutsatira kusowa kwa Meke Mwase, ku timu ya Mighty Mukuru Wanderers chigonjereni ndi timu ya Silver Strikers mu mpikisano wa Airtel Top 8. Mlembi wamkulu wa bungweli, Davie Mpima, wati m’malo monyanyala […]