Zavotereni DPP kuti Mupulumutse Dziko Ku Mbava

Mtsogoleri wa chipani cha DPP a Peter Mutharika wapempha anthu a m’boma la Balaka kuzavotela chipanichi ngati akufuna chitukuko.

A Mutharika ati iwo adzapitiliza zitukuko zonse zimene anaziyamba.

Iwo ati adzapitilizanso kupereka chakudya kwa anthu omwe pakadalipano akhudzidwa ndi njala.

A Mutharika amema anthu a m’delali kuti akhale ndi chiphaso chaunzika komanso adzalembetse mu kaundula wa oponyera voti kuti adzathe kutenga nawo gawo pa chisankhochi.

Related Posts

DPP Blues Rebels Brings Division In

The way Charles Mchacha is castigating the Leader of Opposition in Parliament, Hon Kondwani Nankhumwa, is just testimony enough that Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

LIA Relief Trust Charity Introduced by Zuneth Sattar

by Claire James The LIA Relief Trust is a charitable organisation that works in some of the most impoverished and in Read more

David Bisnowaty former Member Of Parliament for Lilongwe City Centre break silence on political situation in the country

Political cum and former Member Of Parliament for Lilongwe City Centre break silence on political situation in the country https://youtu.be/S20UYlVcHs8

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window