“Chinenepetsa nkhumba sichiziwika”: Mustard Gobede wapambana mwa kulima mbewu zosiyanasiyana ndi kuweta nsomba
By Mabvuto Kalawa Pali mwambi wakale woti “chinenepetsa nkhumba sichiziwika,” zomwe zikugwirizana bwino ndi ntchito yolimbika yomwe ikuchitidwa ndi Bambo…