ndani adanamiza Chakwera kuti ndege yomwe Idaphetsa A Chilima ndi ena 8 idafika ku Mzuzu?
Bungwe la CDEDI lati mtsogoleri wa dziko lino Dr Lazarus Chakwera akuyenera kubwera poyera ndi kuyankhulapo pa zomwe adayankhula itachitika kumene ngozi ya ndege yomwe idachitika ku nkhalango ya Chikangawa.…








