CCTV Lati Zionetsero Zokhudza Ngozi Ya Ndege Ya Ku Chikangawa Zikhalepo
Bungwe la Concerned Citizens Timely Voice (CCTV) laikira kumbuyo ganizo la bungwe la CDEDI lochita ziwonetsero pa nkhani yokhudza ngozi ya ndege ya ku Chikangawa. Malingana ndi kalata yomwe bungweli…









