Malonda Ang’ono Ang’ono, Chips, Mizimbe, Chimanga Azikhoma Msonkho
Boma alipempha kuti liyambe kuika msonkho pa malonda ang’ono-ang’ono monga a chips cha pachiwaya, mizimbe komanso chimanga. Henry Kamkwamba mphunzitsi wa zaulimi komanso zachuma ku sukulu ya ukachenjede ya LUANAR,…








