Timu ya Salima Secondary School yamalizira pa nambala yachitatu mu mpikisano wa African Schools Championship kutsatira kugonjetsa timu ya Sainte Rita 3-1
Blessings Sakala, Ishmael Bwanali komanso Latumbikika Kayira ndi omwe anagoletsa kumbali ya Salima Secondary school
Salima secondary school itenga ndalama zokwana $ 150 ,000 (pafupifupi K150 milllion) pomaliza pa nambala yachitatu