Wednesday, February 28
Shadow

Mmodzi Mwa Candidate Akukapikisana Ku Dpp Convention Hon Bright Msaka

Dpp July uno ili ndi convention komwe madelegetes akukasankha mtsogoleri woti akonze chipani cha Dpp pa kubweletsa anthu onse a Dpp pamodzi.

Mtsogoleri amene akubwelayi akuyenera kugwira ntchito imeneyi ndi adindo a chipani pokonzekera chisankho chomwe chikubwera pa 2025.

Amalawi ambiri ali ndichiyembekezo ndichidwi kuti Dpp ikabwelenso Mboma miyoyo ya amalawi ambiri idzayambilanso kuyenda bwino, pa chifukwa chakuti Tonse alliance inkawawuza anthu kuti ulendowu ndi wakukanani lilibodza ulendo uli wokathelawathela ku gahenah komwe kuli Satan, anthu akukukuta mano tsopano.

-Mwamwayi Mulungu wapeleka Hon Bright Msaka Sc kwa madelegetes a Dpp kuti apulumutse amalawi ku nkhondo ya tonse alliance yomwe yawononga Malawi, munjira zambiri monga:

-Uphawi wadzaoneni.
-Kusowa kwa ndalama za mudziko komanso za mayiko ena .
-Kusowa kwamankhwala mzipatala zonse za Boma.
-Corruption yomwe yakwera chiyambireni dziko lino.
-Nepotism

*Dziko lino kuchoka Mmavuto amenewa likufunika munthu wa experience ya kayendetsedwe ka boma munthuyo ndiye Hon Bright Msaka Sc.

-Munthu amene angayendetse Malawi popanda njenje alipo in the name of Hon Bright Msaka Sc.

Hon Bright Msaka Sc the 7th Malawi president 2025 Boma

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *