Chakwera alibe network -Joyce Banda

IMG 20241101 WA0060

Anzake kunjaku ndi a church omwenso amadalira kupempha.

President wakale wa dziko lino Mai Joyce Banda ati Dr Lazarus McCarthy Chakwera alibe network ya maiko akunja nkana mafuta ndi forex zikusowa mdziko muno.

Iwo amayankhula izi pa pulogalamu ya Kwagwanji pa Times Tv ndi anyamata atatu,Brian Banda, Wonder Msiska komanso Jonna Mpakuku.

Mai Banda adapitiliza kunena kuti mdziko lino liri pa moto wadzaoneni chifukwa a Chakwera alibe maubale ndi ma President akunja (Network alibe) choncho mafuta avutabe.

0 0 votes
Article Rating
Subscribe
Notify of
guest
0 Comments
Oldest
Newest Most Voted
Inline Feedbacks
View all comments
0
Would love your thoughts, please comment.x
()
x