Ndakhutira ndi ntchito yomanga hotela yatsopano – Dr Chakwera
President wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera, wayamika kampani zonse zomwe zidamvana ndikuyika ndalama zawo pamodzi kuti amange Protea Hotel Lilongwe Ryalls. Mtsogoleri wadziko linoyu wati zimenezi zaonetsa mtima odzidalira…