Tinene chalungamo mwayi wathu ndiwochepa tsopano opita ku AFCON – watero Mabedi
Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Flames Patrick Mabedi wati timuyi ili ndi mwayi ochepa tsopano oti ikhoza kudzipezera malo ku ndime yotsiliza yampikisanowa Africa Cup of Nations (AFCON) omwe ukachitikire…









