Iran yati yapambana nkhondo pamene america Ikubwelera M’mbuyo: kusintha kwa mphamvu za dziko la pansi Kwawululika
Yolembedwa ndi Suleman Chitera Dziko la Iran latulutsa mawu amphamvu ponena kuti lapambana nkhondo ya masiku 39 yomwe yasokoneza kwambiri ndale za dziko lapansi, ponena kuti lakakamiza maiko a America…









