Friday, February 23
Shadow

NDIKUFUNA NANKHUMWA AZIMUGWADIRA MUTHARIKA-Namalomba

Mneneri wa Chipani cha DPP a Shadreck Namalomba,awunza Kondwani Nankhumwa kuti asamapange ziganizo payekha akafuna kuchita zinthu.

A Namalomba ati,Nankhumwa akamafuna kuchita chinthu chokhuzana ndi mu chipani cha DPP, aziyamba amufusa kale mtsogoleri wa Chipanichi a Mutharika kamba koti iye ndi wamkulu.

Namalomba amalankhula izi ku mkumano womwe udaliko dzulo ku Mangochi.

A Namalomba ,awunza anthu kuti a Nankhumwa ndi munthu wotsokoneza mu chipani ndipo Peter Mutharika,ndiwokhumudwa ndi zomwe Nankhumwa akuchita.“`

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *