PP yayaka moto kuti buu

FB IMG 1725675634499

President wa chipani cha Peoples Party yemweso ndi m’tsogoleri wopuma wa dziko lino, Mayi Joyce Banda wati mu nthawi ya ulamuliro wawo zinthu m’dziko muno zinkayenda bwino, palibe ankavutika ndi njala komanso anthu sankagona pa filling station.

A Banda ati ndi chipani chawo chokha chomwe chinabweletsa magetsi osazima mu mdziko muno.

0 0 votes
Article Rating
Subscribe
Notify of
guest
0 Comments
Oldest
Newest Most Voted
Inline Feedbacks
View all comments
//otieu.com/4/9370459
0
Would love your thoughts, please comment.x
()
x