Sikuti aliyense amadziwa kuphika… koma ndi nyama za Ekhaya Meats, aliyense amaoneka ngati chef!

IMG 20250702 WA0202

Olo mutakhala kuti sumumatha kuphika, ndiwo zake zikakhala izizi zimakuonetsani ngati dolobe basi! Zimangofuna moto ndi pang’ono pang’ono pa mchere, basi mbale yadzaza!

Nyama yatsopano, yofewa, yokoma

Yabwino kwa ma grill, ma stew, ndi ma braai

Kuchokera ku Ekhaya Meats – komwe okonda nyama amasangalala!

Pezani Ekhaya Meats lero – chifukwa nyama yabwino siingabisidwe!

FreshMeat

MeatLovers

EkhayaMeats

0 0 votes
Article Rating
Subscribe
Notify of
guest
0 Comments
Oldest
Newest Most Voted
Inline Feedbacks
View all comments
0
Would love your thoughts, please comment.x
()
x