Olo mutakhala kuti sumumatha kuphika, ndiwo zake zikakhala izizi zimakuonetsani ngati dolobe basi! Zimangofuna moto ndi pang’ono pang’ono pa mchere, basi mbale yadzaza!
Nyama yatsopano, yofewa, yokoma
Yabwino kwa ma grill, ma stew, ndi ma braai
Kuchokera ku Ekhaya Meats – komwe okonda nyama amasangalala!
Pezani Ekhaya Meats lero – chifukwa nyama yabwino siingabisidwe!