Flames yawuyatsa waku Burkina Faso

FB IMG 1725608391884

Gulu lina latimu yampira wamiyendo yadziko lino ya The Flames lanyamuka ulendo waku Burkina Faso kukatenga mbali mundime yodzigulira malo mumpikisano wa AFCON.

Gululi lanyamuka pabwalo landege ku Lilongwe.

Anyamatawa akukakumana ndi gulu lachiwiri la anzawo ku Ethiopia ndikupitiliza ulendo wawo kudzera m’dziko la Mali.

Timuyi, yomwe yagonja dzulo ndi Burundi, ikumana ndi Burkina Faso lachiwiri lino.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *