Inu mmakonda chani Akasi? Zonse zilipo ndipo zili bwino kwambiri! Kaya mukufuna baked treats kapena natural farm-fresh snacks, Ekhaya Farms Foods yakonzeratu zonse zomwe mungafune!
Timanyadira kukupatsani zakudya zomwe zimakwatiro bwino ndi tiyi nthawi iliyonse – kaya nkumawa, masana kapena madzulo.
Baked Treats? Tili nazo!
Zopangidwa ndi chikondi
Zofewa komanso zokoma
Zosiyanasiyana kuti musankhe zomwe mumakonda
Ekhaya Farms Foods – Zakudya Zachilengedwe. Zakudya Zanu.
Pitani lero! Mukachite enjoy Tea time ndi Zomwera za makonda!