Chigamulo Cha Kamwendo Sichinayende Bwino
Pamene kwangotsala masiku atatu, kuti osewera wa Premier Bet Dedza Dynamos, Promise, akwanilitse masiku omwe akuyenera kubweza K6 million ku timu ya Mighty Mukuru Wanderers kamba kolephereka kwa transfer yake,…








