Azimayi akwiya ndi ganizo la kudula azimuna pa milandu yogwiririra
By Suleman Chitera Azimayi ambiri m’dziko muno akusonyeza kukwiya kwakukulu ndi ganizo lomwe likukambidwa m’Nyumba ya Malamulo loti azimuna opezeka olakwa pa milandu yogwiririra azidulidwa. Malinga ndi azimayiwa, chilango chimenechi…








