Zadziwika kuti mphunzitsi wa Flames, Mario Marinica amalandira pafupifupi K13 million kwacha pa mwezi pomwe mphunzitsi wakale wa timuyi, Meck Mwase ankalandira K1.3 million.
Maganizo anu ndi otani pa momwe bungwe la Football Association of Malawi-FAM komanso boma amayendetsera bwanji nkhani za ma contract a aphunzitsi a Flames? Tinene kuti vuto ndi aphunzitsi a m’dziko muno?