PDP Ikufuna Mashado

Chipani chatsopano cha People’s Development Party – PDP chatsegula khomo kwa omwe akufuna kudzachiyimila ngati aphungu komanso ma-khansala.

M’chikalata chomwe wasindikiza n’neneri wa wachipanichi Rhodes Msonkho PDP yati yachita izi kuti omwe akufuna kudzayimila maudindowa ayifikile.

PDP ndi chipani chomwe angochilembetsa kumene ndipo yemwe akuchitsogelera ndi Kondwani Nankhumwa.

Pamenepa Msonkho wati omwe ali ndi chidwi m’maudindowa afikile PDP kukalembetsa m’kaundula

Related Posts

DPP Blues Rebels Brings Division In

The way Charles Mchacha is castigating the Leader of Opposition in Parliament, Hon Kondwani Nankhumwa, is just testimony enough that Read more

David Bisnowaty Israeli-Born Malawi Parliament Member: Actions, Not Words, Will Change Africa for the Better

Malawi MP David Bisnowaty. How does the Israeli-born son of an eastern European Holocaust survivor end up as a parliament Read more

Mustag Chothia, Sulema Ismael Karim In Land scam

Land remains one area that Malawians know has been heavily abused, characterised by ownership wrangles, not to mention corruption, fueled Read more

David Bisnowaty former Member Of Parliament for Lilongwe City Centre break silence on political situation in the country

Political cum and former Member Of Parliament for Lilongwe City Centre break silence on political situation in the country https://youtu.be/S20UYlVcHs8

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

FDH Launch Islamic Banking Window