Sunday, February 5Malawi's top news source
Shadow

Tag: Kamuzu Chiwambo

Tichepese Mafuta A Galimoto Za Nduna–Watero M’neneri Wa Tonse Alliance

Tichepese Mafuta A Galimoto Za Nduna–Watero M’neneri Wa Tonse Alliance

Stories
Yemwe amayankhulira mgwirizano wa Tonse, Kamuzu Chibambo wati mafuta a galimoto omwe nduna komanso alembi m'boma amalandira atsike kuchoka pa 2000 liters kufika pa mulingo osapyola 750 liters pamwezi ngati njira imodzi yotetezera chuma chadziko lino. Chibambo, yemwenso ndi mtsogoleri wa chipani cha Peoples Transformation-PETRA walankhula izi pa msonkhano wa olemba nkhani munzinda wa Blantyre. Iye watsindika kufunika kokhazikitsa kapena kutsatira mfundo zotukulira chuma kuti dziko lino lidzitha kukhala ndi ndalama zothetsera vuto lakusowa kwa ndalama zakunja. Atakumana atsogoleri a Tonse miyezi yapitayo, Chibambo adauza a Malawi kuti adakambirana mfundo zothetsera mavuto a chuma omwe ayala mphasa m'dziko lino pakadalipano.
PETRA President Kamuzu Chiwambo Fault The Indorsement Of President Chakwera

PETRA President Kamuzu Chiwambo Fault The Indorsement Of President Chakwera

Politics
PETRA, one of the Tonse Alliance partners says it views as premature for the country including the leadership to be drawn into talk about the next elections. The remarks have been made by Kamuzu Chibambo, President for PETRA who says they want President Lazarus Chakwera and Vice President Saulos Chilima not to be involved in the talk about the next polls, describing such involvement as not relevant at this time. According to Chiwambo, what is crucial now for the leadership to do is to address woes that people in the country are facing. He has cited some top promises like job creation more especially among the youth, as appropriate spaces that the leadership needs to be filling due to the current state of affairs. " We don't want our leadership to be involved in this kind of fr...