Sunday, February 5Malawi's top news source
Shadow

Tag: Micheal Usi

Tourism Minister Pledge Government Support Towards Goshen City

Tourism Minister Pledge Government Support Towards Goshen City

National
Minister of Tourism and Culture Michael Usi has pledged government's support towards the Goshen City Project which Prophet Shepherd Bushiri is constructing in Monkey Bay, Mangochi. Writing on his official FacebookPage, the minister says he visited the construction site to appreciate how the project, which has created 4000 jobs already, is progressing and to assure Prophet Bushiri that President Lazarus Chakwera fully supports the project. "Once completed, Goshen City will be one of the greatest tourism sites [in] this part of Africa," he wrote. Prophet Shepherd Bushiri commented on the post saying it has always been his desire to invest in the country. He said: "I thank God for this new government policy that supports development like no other. We will support the President's ...
BWATO SATSITSILANA PAKATI PA NYANJA”-Micheal Usi

BWATO SATSITSILANA PAKATI PA NYANJA”-Micheal Usi

Local
Nduna yowona zokopa alendo yomwenso ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha UTM, Michael Usi awuza President Lazarus chakwera kuti chipani cha UTM chilibe lingaliro lotuluka mu mgwilizano wa Tonse alliance ngakhale pali kagulu kena komwe kakufuna zinthu zitero. A Usi ati kukakamiza chipani cha UTM kutuluka mu mgwilizano wa Tonse mchimodzimodzi kukakamiza munthu kuti atsike mu bwato lili pakati pa nyanja. A Usi alumbila ponena kuti UTM ipitiliza kulemekeza mgwilizano wa Tonse. Iwo ayankhula izi pa mwambo okumbukira mtsogoleri oyamba wa dziko lino Dr Hastings Kamuzu Banda Ku Lilongwe. Poyankhulapo, ndunayi inauzanso Dr chakwera kuti achotse ntchito kagulu kena ka anthu komwe kakufuna kusokoneza boma lake.