Dziko La Malawi Likhale Lotsatira Lamulo- President Chakwera

Muli ndi line Suleman Chitera

Pansi pa utsogoleri wanga ndizaonesesa kuti dziko la malawi lizakhale lotsatira malamulo mopanga kuyang’ana nkhope,

Bambo Brian Banda kucheza ndi President Chakwera