Atsikana Ambiri Atenga Mimba M’boma La Rumphi

CHIWELENGELO CHA ATSIKANA OTENGA MIMBA CHAKWERA KWAMBILI M’BOMA LA RUMPHI

Chiwelengelo chatsikana otenga mimba M’boma la Rumphi Chakwela Kufika pa 2234.

M’neneli wa Chipatala Cha Rumphi a
Banalori Mwamulima ati chiwelengelo ndichoyambila Mmwezi wa January kufika May M’chaka chino.

A Mwamulima ati nambayi ikusonyeza kuti chiwelengelo Chakwela ndi 4% maka pakati pa achitsana omwe ndi achichepele.

Wankulu wampando wa achinyamata a Misheck Msokwa ati Chiwelengelo Chawapatsa mantha.

Chiwelengelochi Chakwela kwambili kusiyana ndichaka chatha Chomwe Chinali 1618 Mmiyezi isanu.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *