NDIZABWEZELESA UMODZI CHIPANI CHA DPP ATERO A BRIGHT MSAKA

a Msaka ati ngati iwo adzasankhidwe kukhala mtsogoleli wa chipani cha DPP mchaka cha 2023, maso awo adzakhala kudzapambana pa chisankho cha utsogoleli wa dziko cha mchaka cha 2025.

Iwo ati ali ndi khumbo lobwezeretsa umodzi mchipani cha DPP akawina pa mpandowu.

Iwo atinso cholinga chawo ndikudza konzanso chuma cha dziko lino chomwe ati chasokonekera pakanali pano.

“Ichi ndichiyambi cha Malawi wokonzeka” Msaka.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *