1 min read

MCM Reviews Code Of Ethics

The Medical Council of Malawi (MCM) has launched the revised Code of Ethics and Professional Conduct for health professionals. Speaking during the launch in Lilongwe, Chairperson for MCM, Professor John Chisi, expressed hope that the new guidelines will curb common professional misconduct by health workers. Meanwhile, Minister of Health, Khumbize Kandodo Chiponda, applauded MCM for […]

1 min read

ONYAMULA MAKALA AMUNJATA KU SALIMA

Apolisi ku Salima amanga bambo wa zaka 30, Yotamu Mapulanga pomuganizira kuti amazembetsa makala ndipo amulandanso galimoto yomwe ananyamulira makalawo ponena kuti inalibe kalata zoyenera. M’neneri wa apolisi m’bomalo, Sub-Inspector Jacob Khembo wati apolisi alanda galimoto ya 15 ton ya mtundu wa Scania yomwe nambala yake ndi KK 7020, yomwe inali yodzadza ndi matumba a […]

1 min read

“Penapake Pakayenda Bwino Zambia Tidya Nayo Bwino”-Dr Chakwera.

President Lazarus Chakwera dzulo lachitatu anapanga mkumano wapadera ndi President wa dziko la Zambia Hakainde Hichilema pambali pa mkumano wa atsogoleri amu bungwe la SADC omwe uli mkati m’dziko la Democratic Republic of Congo. Polemba pa tsamba lawo la Facebook, Dr Chakwera anati iwo ndi a Hichilema anakambilana nkhani zingapo kuphatikizapo ndondomeko yolimbikitsa ntchito za […]