Mabedi Amuchotsa Ntchito

1002192087

Kodi mukuona kuti kuchokochedwa pa ntchito kwa Tate watimu ya Flames, Patrick Mabedi ndi yankho la timuyi?

Osaiwala kuti Mabedi wakhala akuyankhula kuti ngakhale patabwera wina pa mpandowu sipangakhale kusintha ku timuyi.

Nanga FAM iwunike motani pobweretsa mulowa m’malo wake?

Perekani maganizo anu pansipa tiwerenga madzuro ano lero mu pologalamu yathu ya Tchutchutchu pa Nkhani Za Masewero ( 18:30-20:00 hrs).

Mukhozaso kutumiza maganizo anu ku nambala yathu ya 441 ,mulemba mawu akuti Nkhoma FM kusiya kampata ndikulemba maganizo anu kenako kutumiza ku nambalayi.

0 0 votes
Article Rating
Subscribe
Notify of
guest
0 Comments
Oldest
Newest Most Voted
Inline Feedbacks
View all comments
//otieu.com/4/9370459
0
Would love your thoughts, please comment.x
()
x