Chipatala cha Mangochi chilangiza anthu kukhala tcheru ndi matenda a MPox
Wolemba Burnett Munthali Akuluakulu a chipatala cha boma la Mangochi apereka chenjezo lofunika kwa anthu onse m’derali kuti akhale tcheru ndi matenda a MPox, chifukwa mmodzi wapezeka atadwala matendawa ku chipatala cha Koche. Iwo akuwonjezera kuti aliyense akayamba kuona zizindikiro za matendawa ayenera kupita mwachangu kuchipatala kuti athandizidwe. Mneneri wa chipatala cha Mangochi, Harold Kabuludzi, […]
