Chipani cha Odyazake Aibe Mulandu, chavomerezedwa mwalamulo — A Happy Kondowe atsimikiza
By Burnett Munthali Chipani cha Odyazake Alibe Mulandu, chomwe mtsogoleri wake ndi Michael Usi, tsopano chavomerezedwa mwalamulo kutsatira kulembetsedwa kwake mu kaundula wa zipani za dziko lino. Mlembi wamkulu wa chipanichi, a Happy Kondowe, atsimikiza nkhaniyi lero polankhula ndi Zodiak Broadcasting Station, pomwe ananena kuti anthu ofuna kuyimira chipanichi pa mpando wa Uparliamenti ndi U […]
