Chipani cha Malawi Congress Party chatilephera ndipo chinabwera kuzangoononga chuma cha dziko
By Comrade Jumbe Abale ndi Alongo, Tawona ndi maso athu, ndipo tamva ndi makutu athu. Chipani cha Malawi Congress Party chatilephera ndipo chalephera dziko lathu. Zonse zomwe amalonjeza asanalowe m’boma zinali zogwira mtima ngati maloto okoma, koma tawonani lero zonse zija zasanduka kukhala maloto owopysa ndi malawi enieni amoto monga mwadzina lake la dziko lino. […]
