
By Issa Chimwala — Machinga Chisankho cha chipululo cha UDF ku Machinga North East chasokonekera, ngakhale bwalo lalikulu ku Zomba lidalamula kuti chichitike pa 22 July. Izi zatsatira pomwe Denis Maloya, mmodzi mwa omwe akufuna kupikisana, kudzera mwa loya wake Masurool Daud, anakapempha bwalo kuti chipanichi chichititse chisankho cha poyera pambuyo poti chinatsutsa kuti ena apikisanepo. Ngakhale chipanichi chinapereka tsiku…