Aphungu a UTM awachotsa pa magulu a WhatsApp a Boma

1 min read

Kuchokera ku nyumba ya malamulo, aphungu a chipani cha UTM ati atulutsidwa a magulu a mchezo pa What’sApp anjali ya boma

Mwazina aphungu wa dzulo anakana nawo kusintha lamulo lokhudza ma bank

You May Also Like

More From Author

+ There are no comments

Add yours